A Kondwani Nankhumwa atsutsa motemetsa nkhwangwa pamwala kuti iwo amabweretsa chisokonezo ndikunyazitsa utsogoleri wa chipani cha DPP, kotero iwo ati akamang’ala ku bwalo loweluza milandu kaamba kochotsedwa m’chipanichi ndicholinga choti bwalo liwathandize pankhaniyi. A Nankhumwa ayankhula izi kudzera m’chikalata chomwe alemba ndipo iwo ati achotsedwa mchipanichi kaamba kakuti akatakwe ena m’chipanichi akufuna atenge otsogoleri mchipanichi […]
The post Nankhumwa wati akamang’ala ku bwalo lamilandu appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 
