…phungu wadandaulira boma kuthetsa mkangano wa malirewu Pomwe pali kale chiopsyezo cha njala yadzaoneni chaka chino, apolisi komanso anthu a mdziko la Mozambique, pa 17 January, 2024 komaso usiku wa loweruka lapitali, atchetchaso chimanga cha a Malawi pa mkangano wa malire apakati pa dziko lino ndi lawolo ku Makanjira m’boma la Mangochi. Tsamba lino lapeza […]
The post Mkangano wa malire: Anthu aku Mozambique atchetchaso chimanga cha a Malawi ku Makanjira appeared first on Malawi 24.