Likulu la ndende lasamutsidwira ku Lilongwe

Akuluakulu atsimikiza kuti tsopano likulu la nthambi ya ndende lasamutsidwa kuchoka ku Zomba lomwe ndi likulu lakale la dziko lino kupita ku Lilongwe. Izi ndi malingana ndi kalata yomwe nthambi ya ndende yatulutsa yomwe wasainira ndi ofalitsa nkhani wake Senior Superintendent Chimwemwe Mike Shaba omwe ati likulu la nthambi layamba kugwilira ntchito zaka munzinda wa […]

The post Likulu la ndende lasamutsidwira ku Lilongwe appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください