M’modzi mwa anthu omwe athamangitsidwa mchipani chotsutsa boma cha DPP, Mark Botomani, wati zoti iye amuchotsa mchipanichi akungowerenga m’masamba amchezo ndipo iye wati akudikira kalata yochokera ku chipanichi yosonyeza kuti amuchotsa asanapange chiganizo chake pa nkhaniyi. A Botoman ati ngakhale iwo ali ndi chikhulupiliro kuti chikalata chomwe chatuluka chochotsa anthu mchipanichi ndi chenicheni, iwo atemetsa […]
The post Botomani wati akudikira chibaluwa chosonyeza kuti amuchotsa m’chipani appeared first on Malawi 24.