Patangodutsa maola ochepa pomwe anamalira anatchingira nsewu mdipiti wa galimoto za mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera mu nzinda wa Blantyre ndikuyamba kuyimba nyimbo zonyoza mtsogoleriyu, apolisi angapo amchigawo chakum’mwera asamutsidwa pa zifukwa zomwe ena akuti ndi kamba ka chipongwe chomwe tate wafukoyu wachitilidwachi. Lachisanu lapitali, kunali chifwilimbwiti pa mphambano ya HHI munzinda wa […]
The post Apolisi asamutsidwa anamalira atatchingira nsewu mdipiti wa Chakwera appeared first on Malawi 24.