Phungu watsekulira chipinda chophunziliramo m’dera lake

Phungu wa nyumba ya malamulo mchigawo chapakati m’boma la Salima watsekulira chipinda chophunziliramo ndi kupereka mayunifolomu kwa ophunzira okwana 100 pa sukulu yapulayimale ya Demera yomwe ili mdera la mfumu yayikulu Maganga m’bomali. Malingana ndi Phunguyi, a Kapisen Phiri, wati wamanga chipinda chophunziliramochi kaamba koti pasukuluyi padalibe zipinda zophunzililaramo zokwanira. Chipindachi chamangidwa ndi thandizo lochokera […]

The post Phungu watsekulira chipinda chophunziliramo m’dera lake appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください