Wachiwiri kwa mtsogoleri wa UDF watuluka chipani

Wachiwiri wa mtsogoleri wa chipani cha United Democratic Front (UDF) mchigawo chakum’mawa Hasheem Banda watula pansi udindo wake komanso watuluka muchipanichi. Hasheem Banda wanena zakutula pansi udindo wake komanso kutuluka muchipani cha UDF pa msonkhano wa olemba nkhani omwe adachititsa mu mdzinda wa Zomba. Iye wati watuluka mu chipani cha UDF potsatira zomwe zidachitika pa […]

The post Wachiwiri kwa mtsogoleri wa UDF watuluka chipani appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください