Wanjatidwa kamba kogwililira ana atatu a zaka zinayi

Mnyamata wina opanda dambisi wazaka 18 wavekedwa zibangiri ndikusungidwa mkambolimboli ndi apolisi m’boma la Thyolo kaamba komuganizira kuti adagwililira ana akazi atatu a zaka zinayi zakubadwa.. Nkhani yonse ikuti nyamatayu yemwe dzina lake ndi Milwad Stanley adachita zadamazi ndi ana atatuwa dzana pa 17 January cha ku mtsinje wa Namichimba komwe adakumana ndi anawa chakumadzulo. […]

The post Wanjatidwa kamba kogwililira ana atatu a zaka zinayi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください