Akuluakulu oyendetsa timu ya Wanderers awachotsa

Zatsimikizika kuti mamembala a bhodi ya timu ya mpira wa miyendo ya Mighty Mukuru Wanderers awachotsa. Wapampando wa timuyi a Thomson Mpinganjira atsimikiza za nkhaniyi. Mu chikalata chomwe wasayina ndi mtsogoleriyu chikufotoka kuti izi zadza kamba ka maganizo a akulualuku omwe ndi eni makampani omwe amathandizira kuyendetsa timuyi. “Kamba ka kusinthidwa kwa adindowa, chilichose choyenera […]

The post Akuluakulu oyendetsa timu ya Wanderers awachotsa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください