Bwalo la Principal Resident’s Magistrate ku Zomba layamba kumva mulandu wa mkulu wa Bungwe la Malawi First a Bon Kalindo omwe akuwaganizira kuti adayambitsa chisokonezo pa ziwonetsero zomwe adachititsa mu Mzinda wa Zomba pa 23 November chaka chatha. Apolisi atsekulira mulandu a Bon Kalindo powaganizira kuti adayambitsa chisokonezo panthawi yomwe adachititsa ziwonetsero mu mwezi wa […]
The post Bwalo la milandu ku Zomba layamba kumva mulandu wa a Bon Kalindo appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 