Khoti la Euthini, m’boma la Mzimba lagamula Martha Chaula wa zaka 47, kukakhala kundende kwa miyezi 18 popezeka wolakwa pa mulandu wofuna kuba khanda. Bwaloli linamva kuti mayiyu anachita izi pofuna kusangalatsa mamuna wake, yemwe wakhala akuuza mkaziyo kuti amuberekere mwana ngati akufuna kuti amumangire nyumba komanso kumuyambitsira mabizinesi osiyana siyana. Bwaloli linamvanso kuti mayiyu […]
The post Mai wofuna kuba mwana amugamula kukakhala ku ndende miyezi 18 appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 