M’modzi mwa oyimba odziwika bwino ku ku Malawi, Katelele Ching’oma, watisiya. Oyimbayu wamwalira lero ku chipatala cha Kamuzu Central ku Lilongwe komwe anatengeredwa. Mchimwene wake wa oyimbayu, a Elvis Ching’oma, wati Katelele amadwala nthenda yokhudza chiwindi. Moses Makawa, yemwe anali mnzake wa Katelele wati oyimbayu anagonekwdwa ku chipatala masiku atatu apitawa. “Amadwala inde koma masiku […]
The post Katelele Ching’oma watisiya appeared first on Malawi 24.