Apolisi mu mzinda wa Lilongwe ati akusakasaka atsizinamtole omwe athyola ofesi ya wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima ku Capital Hill ku Lilongwe momwe akuti abamo bisiketi ndi inki ya “printer”. A Salome Zgambo omwe ndi ofalitsa nkhani ku polisi ya Lingadzi munzindawu, awuza nyumba zina zofalitsa nkhani mdziko muno kuti akuganizira […]
The post Mbava zathyola ofesi ya Chilima ku Lilongwe appeared first on Malawi 24.