A Chakwera ati zomanga zitsate ma sitandadi

Poyendera nyumba za a chitetezo  zomwe akuzimanga ku Mitole  m’boma la Chikwawa,   mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wati Nyumba zomangidwa zikuyenera kutsata ndondomeko zabwino  zomangira kuti zizikhala zolozeka. Polankhula m’mau awo m’mawa  wa lero, a Chakwera ayamikila ntchito yomanga nyumba za a polisi zokwana makumi atatu (30) yomwe ili mkati  m’bomali ndipo ati ntchito […]

The post A Chakwera ati zomanga zitsate ma sitandadi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください