Inu azibambo  a COSOMA mukundisala bwanji? Wafunsa Jetu

Jetu walira chokweza pamene bungwe la Copyright Association of Malawi (COSOMA) silidamupatseko yachipuputa misonzi pamene bungweli lapereka makobidi kwa oyimba osiyanasiyana mdziko muno ndipo iye akufunsa kuti a COSOMA akumusala bwanji? Jetu wayankhula izi kudzera munkanema yemwe Malawi24 yaona ndipo izi ndi zomwe wafotokoza: “Eee ndikufunseni inu azibambo aku COSOMA ine ndi Jetu azanga onse […]

The post Inu azibambo  a COSOMA mukundisala bwanji? Wafunsa Jetu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください