Kudya thukuta lawo: Oyimba akusimba lokoma; Njuchi, Driemo apakula pakulu

Zoti mwezi wa January umakhala ndi masiku ochuluka zedi, oyimba ambiri siziwakhudza kamba koti bungwe la COSOMA lawaombola powapatsa dipo la thukuta lawo; komatu awiri obadwa m’ma 2000-wa asadabuza achiyamba kale poti ndiomwe atapa phwamwamwa. Lero Lachitatu, Bungwe la Copyright Society of Malawi (COSOMA) lagawa ndalama zokwana K505 million kwa anthu aluso mdziko muno ndipo […]

The post Kudya thukuta lawo: Oyimba akusimba lokoma; Njuchi, Driemo apakula pakulu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください