Malingana mkuona kwa a Sylvester Namiwa yemwe ndi mkulu wa bungwe la CDEDI, ati ofesiyi ya mtsogoleri wachiwiri mdziko muno siikuwoneka ntchito yeni yeni yomwe ikugwira kotero iwo ati mpofunika kuti dziko lino liwunikenso ngati ofesiyi ndiyofunika kapena ayi A Namiwa anena izi poona kuti ofesi ya mtsogoleri wachiwiriyu kuti igwire ntchito imadalira kupatsidwa mphamvu […]
The post Awunikirenso ngati ofesi ya wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino ndiyofunika, watero Namiwa appeared first on Malawi 24.