“Chakwera amange chipatala china nkuchitchula dzinalo” – atelo a Malawi ena

Anthu ena mdziko muno awonetsa kusagwirizana ndi zomwe mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera achita posintha dzina la chipatala cha Phalombe kukhala John Chilembwe ndipo ambiri alangiza mtsogoleriyu kuti mwana omupeza sumamusintha dzina, umangolimbikira, n’kubala wako, n’kumupatsa dzina ukufunalo. Izi zikudza pomwe a Chakwera Lolemba pa 15 January, 2024 alamula kuti chipatala chachikulu cha […]

The post “Chakwera amange chipatala china nkuchitchula dzinalo” – atelo a Malawi ena appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください