Boma lati ligawa masikito otetezera ku udzudzu mzigawo zonse m’dziko muno pofuna kuthana ndi nthenda ya malungo yomwe ikadaperekabe chiwopsezo chachikulu pa umoyo ndipo ntchitoyi igwilika ndi thandizo la ndalama pafupifupi 84 biliyoni kwacha lomwe ipeleke ndi bungwe la Global fund. Malingana ndi m’modzi mwa akuluakulu ku nthambi ya unduna wa za umoyo mdziko muno, […]
The post Boma likuyembekezeka kugawa masikito mdziko muno appeared first on Malawi 24.