Kuchepa kwa malipiro kukukolezera mchitidwe okuba mu ma kampani a amwenye

Ogwira ntchito mu ma kampani a amwenye mu mzinda wa Blantyre akuti akukakamikizika kuyamba mchitidwe ozembetsa katundu m’malo ogwirira ntchito ndi kumakagulitsa chifukwa cha kuchepa kwa malipiro. M’modzi mwa ogwira ntchito wina yemwe anati tisamutchule dzina anati ndalama yomwe amalandira imakhala yochepa zomwe zimakhala zovuta kusamalira mabanja awo ndipo zimayambitsa anthu ogwira ntchito kukhala ndi […]

The post Kuchepa kwa malipiro kukukolezera mchitidwe okuba mu ma kampani a amwenye appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください