DODMA yapereka thandizo kwa anthu okhudzidwa ndi kusefukira kwa madzi ku la Dowa

Kutsatira kusefukira kwa madzi komwe kwakhudza anthu m’boma la Dowa ku Mponera, bungwe loona za ngozi zogwa mwadzidzi la DODMA dzulo lapereka thandizo losiyasiyana kuphatikizapo ufa, mabulangete, mabigiri, matenti, komanso nyemba. Bungweli lapereka mabulangete okwana 139, ufa matumba okwana 37, nyemba zolemera ma kilogiramu 10 kubanja lililonse, matenti, komanso ma mabigiri okwana 37. A Mercy […]

The post DODMA yapereka thandizo kwa anthu okhudzidwa ndi kusefukira kwa madzi ku la Dowa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください