Masewero a AFCON awonetsedwa pa kanema wa SuperSport

Kampani ya MultiChoice  yatsimikizira anthu  okonda masewero a mpira mdziko muno kuti mpira wa chaka chino wa Africa Cup of Nations (AFCON) ukhala ukuonetsedwa pa kanema wa Super Sport Chikalatachi chadza pamene masiku apitawo panali nkhawa yoti SuperSport sionetsa masewelowa pakanemayu. Ndipo malingana ndi kalata yomwe kampaniyi yatulutsa,  masewera onse okwana 52 akhala akuonetsedwa pa […]

The post Masewero a AFCON awonetsedwa pa kanema wa SuperSport appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください