Malingana ndi kukwera kwa misonkho ya galimoto m’dziko lino, bungwe lomwe limayang’anira zokhudza galimoto zowilitsidwapo kale ntchito la Used Car Dealers Association of Malawi, lati nkofunika kuti boma liunikenso misonkho yomwe bungwe la MRA likumalipiritsa ponena kuti misonkhoyi ndi yokwera kwambiri. Ganizoli ladza kutsatira mavuto omwe anthu ochita malondawa akukumana nawo mdziko muno ponena kuti […]
The post Boma lapemphedwa kuti liunikenso misonkho ya galimoto appeared first on Malawi 24.