M’malawi okhala ku Kuwait akufuna kupikisana nawo pa mpando wa mtsogoleri wadziko lino

Nzika ya dziko lino a Eddie Longwe omwe amakhala m’dziko la Kuwait ati ali ndi chidwi chopikisana nawo pa zisankho za mtsogoleri wadziko lino zomwe zikuyembekezeka kuchitika chaka chamawa. A Longwe auza Malawi24 kuti iwo ndiwokonzeka kuombola amalawi omwe pakadali pano akukumana ndimavuto osiyanasiyana mu ulamuliro wa presidenti Lazarus Chakwera. Iwo ati ali ndinfundo zikuluzikulu […]

The post M’malawi okhala ku Kuwait akufuna kupikisana nawo pa mpando wa mtsogoleri wadziko lino appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください