Khuda Myaba yemwe pano alibe timu yomwe akuonetsera ukatswiri wake, watutumutsa gulu pomwe wanena kuti alibe ganizo losewera mu ma timu a Mighty Mukuru Wanderers komanso FCB Nyasa Big Bullets ponena kuti matimu onsewa sangakwanitse kumulipira pa mwezi. Myaba wauza tsamba lolemba nkhani za masewero la ‘Wa Ganyu’ kuti mphekesera zomwe zikumveka kuti iye akukambirana […]
The post Sindikupita ku Wanderers kapena Bullets, sangakwanitse kundilipira – watelo Khuda Myaba appeared first on Malawi 24.