Mnyamata wa zaka 18 zakubadwa yemwe anali mu fomu 1 wafa atadzinjatilira pa mtengo ku Mponela m’boma la Dowa kamba kakuti amadzudzulidwa pakhalidwe lake lochita maubwezi ndi atsikana osiyanasiyana. Nkhani yonse ikuti mnyamatayu yemwe dzina lake ndi Hastings Chakufuma, amakhala ndi azakhali ake ndipo anamudzudzula kamba ka khalidwe lopanga zibwenzi ndi atsikana osiyanasiyana. Lolemba pa […]
The post Mnyamata wadzimangilira kamba kodzudzulidwa appeared first on Malawi 24.