Ngati njira imodzi yofuna kupewera matenda a chimanga omwe agwa mdziko la Tanzania kuyambukira mdziko muno, boma la Malawi lati likagayitsa chimanga chomwe linalanda anthu ena omwe amafuna achilowetse mdziko muno. Izi zikudza pomwe boma la Malawi kumapeto a chaka chatha linaletsa aliyese kulowetsa m’dziko muno chimanga chochokera mdziko la Tanzania komanso Kenya ati pofuna […]
The post Boma ligayitsa chimanga chomwe linalanda chochokera ku Tanzania appeared first on Malawi 24.