…ati wofesa amayembekezera kukolora …ati BBC ikuwawidwa ndi kukula kwa mpingo ngakhale TB Joshua anamwalira Akuluakulu a mpingo wa Synagogue Church of All Nations (SCOAN) ku Nigeria, ati anthu asatekeseke ndi nkhani yomwe wayilesi ya BBC yatulutsa yokhudza malemu Mneneri TB Joshua ponena kuti nkhani zomwe wayilesiyi ikufalitsa, ndizopeka ndipo mpingowu sukuwadziwa anthu omwe amafusidwa […]
The post Musawamvere, nkhanizo ndizopeka – SCOAN yayankha pa zomwe BBC yatulutsa za TB Joshua appeared first on Malawi 24.