Timu ya Mighty Mukuru Wanderers yapulumukira dzenje lokumbakumba pomwe bungwe loyendetsa mpira mdziko muno la FAM lauza timuyi kuti isachimwenso kwa chaka chimodzi kuti isalandile chilango chomwe bungweli linapeleka choti Wanderers isatenge nawo gawo pa mipikisano yonse m’dziko muno kamba konyanyala masewero a chikho cha Airtel Top 8. Pa 6 December chaka chatha, timu ya […]
The post Pita koma usakachimweso: Wanderers ayiletsa kusewera mpira ku Malawi koma isewerabe appeared first on Malawi 24.