Akhristu a Mpachika CCAP adzudzula m’busa Ntepiha kuti akugwiritsa ntchito zithumwa pofuna kuthana ndi atsogoleri

Akhristu a mpingo wa Mpachika CCAP m’mzinda wa Blantyre adzudzula m’busa wawo, a Raphael Ntepiha, kuti akugwiritsa ntchito zithumwa pofuna kuthana ndi atsogoleri ampingo omwe akutsutsana ndi maganizo awo. Amene watipatsa nkhaniyi akuti nkhondo ya pakati pa akhristu ndi abusawa inafika pachimake Lolemba lathali pomwe abusa a Ntepiha adakawaza mankhwala kuzungulira tchalitchi uku akutchula maina […]

The post Akhristu a Mpachika CCAP adzudzula m’busa Ntepiha kuti akugwiritsa ntchito zithumwa pofuna kuthana ndi atsogoleri appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください