Patadutsa zaka ziwiri ndi miyezi ingapo chimwalilireni mneneri TB Joshua ku Nigeria, wayilesi ya British Broadcasting Corporation (BBC) yabweletsa poyera zotsatira za kafukufuku yemwe inapanga pa zoipa zomwe a Joshua amapanga monga kugwililira amayi ndi atsikana ndi kuwakakamiza kuchotsa mimba komanso kupanga zozizwitsa zabodza. Koma nkhaniyi yakwiyitsa anthu ochuluka m’mayiko a mu Africa omwe akuti […]
The post Tisiyileni wathuyo pangani zanu – BBC yakwiyitsa anthu a ku Africa pa nkhani ya malemu TB Joshua appeared first on Malawi 24.