Boma kudzera kwa mlangizi wake pa za malamulo lati likukonza zoti likasume kutsutsana ndi chigamulo choti lipeleke ndalama yokwana K103 miliyoni kwa a Brian Banda ngati chipepeso powachotsa ntchito ya mneneri wa mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera. M’mwezi wa August mchaka cha 2020, a Banda omwe pano akugwira ntchito ngati mtolankhani ku Times […]
The post Boma silikugwirizana ndi chipepeso cha K103 miliyoni kwa Brian Banda appeared first on Malawi 24.