Potsatira zionetso zomwe mtsikana wina Hendrina Kamenya anachita ku maofesi aboma munzinda wa Lilongwe Lachinayi zokhudza ndalama za chipukuta misozi za malemu bambo lake, lero Lachisanu boma lapeleka wawo lina la ndalamazi. Mtsikanayu yemwe ndiwochokera m’boma la Mwanza, kuyambira Lachinayi m’mawa anali ku maofesi a boma ku Capital Hill ku Lilongwe komwe anachita m’bindikilo pofuna […]
The post Mtsikana wa zionetsero wapatsidwa ndalama za malemu bambo ake appeared first on Malawi 24.