Adindo awapempha kuchita machawi kuthetsa kusamvana pankhani ya malire a dziko lino ndi dziko la Mozambique ku Mangochi pomwe akuti apolisi ndi anthu a m’dziko la Mozambique atchetcha chimanga cha a Malawi ku midzi ina kudera la mfumu yaikulu Makanjira m’bomalo ponena kuti malowo ali m’dziko lawo la Mozambique. Malingana ndi zomwe tsamba lino lapeza, […]
The post Mkangano wa malire a Malawi ndi Mozambique wavuta ku Mangochi appeared first on Malawi 24.