Dziko la Zambia, lomwe ndi neba wa Malawi, lati sukulu m’dzikoli zikhalabe zotseka mpaka pa 29 January, 2024 kamba ka muliri wa cholera womwe wabuka dzikolo. Chikalata chomwe unduna wa za maphunziro mogwirizana ndi unduna wa za umoyo watulutsa chati sukulu zonse zaboma komaso zomwe si za boma zaimitsidwa kaye ngati njira imodzi yochepetsa kufala […]
The post Sukulu ku Zambia zikhalabe zotseka kamba ka Cholera appeared first on Malawi 24.