Gulu la pa tsamba la mchezo lathandiza odwala pa chipatala cha Salima

Ngati njira imodzi yokondwelera nyengo ya khilisimisi komanso chaka chatsopano, gulu la pa tsamba la mchezo la WhatsApp la ‘Malawian  Gossip and Scandals’ linakachezela odwala pa chipatala chachikulu cha boma la Salima. Gululi lapereka katundu osiyanasiyana wa ndalama pafupifupi K500  sauzande  kwa ana omwe agonekedwa pa chipatalachi ndipo akulandira thandizo la mankhwala. Poyankhula atapereka thandizoli, […]

The post Gulu la pa tsamba la mchezo lathandiza odwala pa chipatala cha Salima appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください