A Malawi konzekani. Tsopano kukhala kupha makwacha kudzera pa tsamba la mchezo la Fesibuku komanso pa YouTube kuyambira chaka chomwe tichiyambe mawali cha 2024. Izi zili chomwechi malingana ndi zomwe wanena mkulu wa bungwe la MACRA a Daudi Suleiman. Iye wati tsopano dziko la Malawi lilandira chilolezo choti anthu azitha kupeza ndalama kudzera pa masambawa. […]
The post Anthu a ku Malawi ayamba kupha makwacha pa YouTube ndi Fesibuku mu 2024 appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 