Mukaona amuna kapena akazi ochita maukwati okhaokha gendani, watero pulezidenti wa ku Burundi

Mtsogoleri wadziko la Burundi Evariste Ndayishimiye yemwenso ndi mkatolika, wadzudzula mayiko a azungu kamba kolimbikitsa ma ufulu oti amuna kapena akazi azikwatirana okhaokha. Mkunena kwake wati izi ndizonyasa komanso zamalawulo kotero oterewa akapezeka aziyikidwa mbwalo la masewero ndikuponyedwa miyala. Iye wadzudzula mayiko a azungu omwe amalimbikitsa mayiko ang’onoang’ono kuti alole maukwati a amuna kapena akazi […]

The post Mukaona amuna kapena akazi ochita maukwati okhaokha gendani, watero pulezidenti wa ku Burundi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください