Pitani ndakukhululukirani koma musakachimwenso: Chakwera wakhululukira akaidi

Akayidi okwana 48 tsopano akhala akusimba lokoma kutsatira mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera  wakhululukira ndikumasula akayidiwa mnyengo ino  yachikondwerero cha khilisimasi komanso chaka chatsopano. Malingana ndi chikalata chomwe atulutsa a Oliver Kumbambe yemwe ndi mlembi wamkulu muunduna wazachitetezo, mtsogoleri wa dziko lino wakhululukira akayidiwa omwe tsopano agwira theka lazaka zomwe khothi lidawagamula. Mwa akayidi […]

The post Pitani ndakukhululukirani koma musakachimwenso: Chakwera wakhululukira akaidi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください