Sukulu ya University of Livingstonia yakweza fizi

Sukulu ya ukachenjede ya University of Livingstonia (Ekwenden Campus) yalengeza kuti yakweza sukulu fizi ndipo izi zikhudza ophunzira amene akudzayamba kumene komanso omwe omwe akupitiliza maphunzilo awo pasukuluyi. Malingana ndi chikalata chomwe sukuluyi yatulutsa, kusinthaku kuyamba mu January 2024, mwezi omwe uyambike sabata la mawa lolemba. Ndipo kubweraku kuli motere: Ophunzira omwe ndi okhalira pasukulu […]

The post Sukulu ya University of Livingstonia yakweza fizi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください