Apolisi ku Kasungu apempha anthu oyendetsa galimoto kuti ‘ ‘asayiponde fadah’ komanso asayendetse atapapira bibida komanso mankhwala ozunguza bongo pofuna kuti aliyense alowe mchaka chatsopano cha 2024 ndi moyo. Yemwe ndi komishonala wa apolisi mchigawo chapakati ku m’mawa a Rhoda Manjolo ndi omwe ayankhula izi kumadyelero omwe amachitikira pa sukulu ya sekondale ya Loyola m’bomali. […]
The post ‘Musayiponde fadah’ mutapapira mkalabongo komanso mankhwala ozunguza bongo appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 