Apolisi ku Kasungu atsekera mchitokosi anthu atatu omwe akuwaganizira kuti anapha bambo wa zaka 38 yemwe adamugwira akuba nkhuku. Anthuwa, ndi a Simon Genesis a zaka 40, Kachule Gwilire, a zaka 53 Komanso a Chrisy Genesis a zaka 53, onsewa a m’mudzi mwa a Genesis mfumu yaikulu Kasichi m’bomali. Malingana ndi a Joseph Kachikho omwe […]
The post Anthu atatu amangidwa kamba kokupha munthu yemwe anagwidwa akuba nkhuku appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 