Kampani ya mafoni a m’manja ya Airtel Malawi yati kuyambira sabata ya mawa itsitsa ndi 1 kwacha mitengo yomwe makasitomala ake amalipira akamayimbira lamya kapena kutumiza mauthenga ku ma netiweki ena. Izi ndi malingana ndi kalata yomwe kampani ya Airtel Malawi yatulutsa Lachinayi pa 28 December, 2023, yomwe ikusonyeza kuti mitengo ya tsopanoyi ikuyembekezeka kuyamba […]
The post Airtel itsitsa mtengo oyimbira ku manetiweki ena appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 
