A Nankhumwa asankha Mneneli wawo

Mtsogoleri wa mbali ya otsutsa boma  ku nyumba ya Malamulo muno mu Malawi a Kondwani Nankhumwa asankha phungu wa Nyumba ya Malamulo wa ku  dela la Mangochi Monkey-bay a Raph Jooma kukhala owayankhulira. Malingana ndi chikalata chomwe chatuluka  lero pa 28 December 2023 ndipo  chasainidwa ndi ndi Mlembi wawo wamkulu a Dorothy  Kabango ati ntchito […]

The post A Nankhumwa asankha Mneneli wawo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください