Arava Farm yomwe ndi imodzi mwa kampani zomwe zatenga a Malawi kukagwira ntchito mdziko la Israel, yati anthu mdziko muno asadere nkhawa za umoyo wa azibale awowa ponena kuti anthuwa akugwira ntchito mosangala kwambiri, ndipo yatsutsa mphekesera zoti m’Malawi m’modzi waombeledwa ndi gulu la nkhondo la Hamas. Wayankhula izi ndi m’modzi mwa akuluakulu a kampani […]
The post A Malawi akusangalala kuno, palibe waombeledwa – yatelo kampani yomwe yalemba a Malawi ntchito ku Israel appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 