Wapha mzake pa khilisimasi pomumenya ndi khasu m’mutu

Apolisi ku Kasungu anjata bambo wina wazaka 29 wina yemwe akumuganizira kuti anapha mzake wazaka 28 dzana pa khilisimasi pomumenya ndi khasu m’mutu. Malingana ndi mneneri wa apolisi m’bomali a Joseph Kachikho ati bambo yemwe akumuganizira kuti adapha mzakeyu ndi a Yamikani Mlotha ndipo ophedwayu ndi a Paul Banda. Nkhani yonse ikuti awiliwa anapita ku […]

The post Wapha mzake pa khilisimasi pomumenya ndi khasu m’mutu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください