Zina ukamva ngati kumaloto ndithu. Apolisi m’boma la Kasungu amanga mfumu Mwimira yazaka 52 kamba kogwilira mdzukulu wake wazaka 16 ndikumpatsanso pathupi. Malingana ndi mneneri wa apolisi m’bomali a Joseph Kachikho, makolo amwanayu anadabwa kumuona mwanayu akuwoneka kuti ali ndi pathupi koma mwanayu samanena yemwe anampatsa pathupipo. Atamupanikiza ndi mafunso, mwanayu adawulula kuti pathupipo adampatsa ndi […]
The post Malaulo: Mfumu yapereka pathupi kwa mwana wazaka 16 appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 