Ulimi wa mthilira ndi omwe ungapulumutse Malawi ku vuto lakusowa kwa chakudya, atero akatswiri

Pamene madera ambiri dziko lino akhudzidwa ndi vuto losowa mvula yokwanira, pali chiopsezo choti dziko lino likhala lopanda chakudya chokwanira chaka cha mawa. Koma akatswiri pa nkhani za ulimi ati boma likuyenera kulimbikitsa alimi kuti azichita ulimi wa mthilira komanso alangiza alimi dziko lino kutsatira njira za makono za malimidwe ndi kugwiritsa ntchito mbeu zosachedwa […]

The post Ulimi wa mthilira ndi omwe ungapulumutse Malawi ku vuto lakusowa kwa chakudya, atero akatswiri appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください