Gulu la achinyamata omwe amachita masewero oyendetsa galimoto mochititsa kaso a motorsport-spinning pachizungu mumzinda wa Blantyre apempha boma kuti liyesetse kuyikapo chidwi pofuna kutukula masewerowa m’dziko muno ponena kuti ndiofunika kwambiri. Izi zanenedwa dzulo ku Chilobwe mu mzindawu komwe gululi lomwe likutchedwa Spinners Nest Motorsport linali ndi chilawitso chamasewerowa. M’mawu ake Geoffrey Jarid yemwe ndiwapampando […]
The post Boma alipempha kuyikapo chidwi potukula masewero oyendetsa galimoto appeared first on Malawi 24.