Apolisi ku Ndirande tsopano akhala akusimba lokoma pamene nduna ya zachitetezo a Kenneth Zikhale Ng’oma lero yatsekulira nyumba zamakono zokwana 20 zomwe boma la a Lazarus Chakwera lamanga mgawo la nyumba 10,000 zomwe zikhale zikumangidwa m’dziko lino. Kutsatira lonjezo lomwe adachita a Chakwera mchaka cha 2020, pofika lero bomali lamangapo nyumba zokwana 1028, ndipo 20 […]
The post Boma lapereka nyumba 20 kwa apolisi m’dziko muno appeared first on Malawi 24.